DCCMS_Malawi (@dccmsm) 's Twitter Profile
DCCMS_Malawi

@dccmsm

Department of Climate Change & Meteorological Services page. Updates on #Malawi Weather, Climate, Alerts & News for informed decisions bit.ly/m/dccms

ID: 1246703055216803840

linkhttps://www.metmalawi.gov.mw calendar_today05-04-2020 07:36:35

1,1K Tweet

3,3K Followers

689 Following

DCCMS_Malawi (@dccmsm) 's Twitter Profile Photo

24 May 2025 ☁️☁️☁️Kwacha kwa mitambo ndikozizira m'madera ambiri moti ndi madera ochepa okha komwe dzuwa likuonekako. M'bandakucha wa lero ku Dedza ndikomwe kunazizira kwambiri ndi madigiri 10.6. Tisaiwale kuti nyengoyi ikupitilira mawa lamulungu pa 25 May 2025. #StayWarm

24 May 2025

☁️☁️☁️Kwacha kwa mitambo ndikozizira m'madera ambiri moti ndi madera ochepa okha komwe dzuwa likuonekako. M'bandakucha wa lero ku Dedza ndikomwe kunazizira kwambiri ndi madigiri 10.6. Tisaiwale kuti nyengoyi ikupitilira mawa lamulungu pa 25 May 2025.

#StayWarm