@davidmpha
Eyes Forward 🦾
ID: 1209771554000777217
calendar_today25-12-2019 09:44:07
692 Tweet
1,1K Followers
1,1K Following
23 days ago
Anthu otchukawa pa interview, kuwafunsa kuti what's your favorite meal? Akuti ine mmakonda nsima ya nkhwani otendera, utaka kapena therere. Apopo ndiye mwanditha. Bodza, kumamasuka, awuzeni mmakonda mpunga wanyama inu😂 sivuto bro. Sikususukanso ayi. Sikukula movitikanso ayi🤣🙌