Onjezani Kenani(@onjezani) 's Twitter Profileg
Onjezani Kenani

@onjezani

The truth alone will triumph.

All tweets here are my personal views and not my employer's or anybody else's.

ID:1350757100251729921

calendar_today17-01-2021 10:49:38

2,8K Tweets

35,8K Followers

2,5K Following

Onjezani Kenani(@onjezani) 's Twitter Profile Photo

Boma lakhulukira anthu ngongole zawo amene anatenga ngongole zokwana K6 biliyoni ku bungwe lija lokongoza ndalama la National Economic Empowerment Fund (NEEF).

account_circle
Onjezani Kenani(@onjezani) 's Twitter Profile Photo

This is a great innovation by the ministry responsible for culture - a national calendar for cultural events. Here is a snapshot for the month of May. This will help those interested to plan for the events they wish to attend. Well-done.

Meanwhile, ku Mzuzu University, nkhani yavuta ndi Sexually Transmitted Grades, malinga ndi nyuzipepala ya Nation ya lero. Akuti m'phunzitsi wina wakhala akukakamiza ana asukulu a chitsikana kuti agone nawo ngati akufuna akhoze phunziro lake.

account_circle
Onjezani Kenani(@onjezani) 's Twitter Profile Photo

Malinga ndi ripoti la MIJ, Airtel yakweza mitengo. Tenifolo ya mawu 15 pelesenti, data 23 pelesenti, ndipo ma meseji a SMS 20 pelesenti.

account_circle
Onjezani Kenani(@onjezani) 's Twitter Profile Photo

Good news. Cost of living yatsika, malinga ndi ripoti la Centre for Social Concern. Makamaka ku Lilongwe yatsika ndi 16 pelesenti, ku Mangochi 14 pelesenti, koma Blantyre, Zomba ndi Mzuzu yatsika mocheperapo, cha m'ma 3 pelesenti umu.

account_circle
Onjezani Kenani(@onjezani) 's Twitter Profile Photo

Meanwhile, mu nkhani zina: Maneba akumanga international airport ku Chipata. Akufuna kulimbikitsa cultural tourism, makamaka ndi ma ceremony ngati Kulamba.

account_circle
Onjezani Kenani(@onjezani) 's Twitter Profile Photo

Meanwhile, on 8 Apr Ethiopian Airlines CEO and COO worked as cabin crew on a flight to Cairo to celebrate 78 yrs of existence. Passengers received complimentary WiFi. ET's growth since 2010 includes doubling its fleet and destinations, becoming Africa's largest carrier. Congrats.

account_circle
Onjezani Kenani(@onjezani) 's Twitter Profile Photo

This is totally unacceptable. Stop intimidating journalists. Release MacMillan Mhone now, now, now, not tomorrow.

This is totally unacceptable. Stop intimidating journalists. Release MacMillan Mhone now, now, now, not tomorrow.
account_circle
Onjezani Kenani(@onjezani) 's Twitter Profile Photo

The Malawi Revenue Authority beat its 2023/24 target after collecting K2.2 trillion in taxes, K5 billion more than its target. Congratulations.

account_circle
Onjezani Kenani(@onjezani) 's Twitter Profile Photo

Malawi has been named the seventh best governed country on the continent. Number 1 was Mauritius. Congratulations to President Chakwera, the cabinet, Members of Parliament and the Judiciary. We must be proud of ourselves.

account_circle
Onjezani Kenani(@onjezani) 's Twitter Profile Photo

Ndikanena ine za pasipoti, a tidyenawo ena akumawona ngati ndikunama. Dziwerengereni nokha m'Malawi News yalero.

Ndikanena ine za pasipoti, a tidyenawo ena akumawona ngati ndikunama. Dziwerengereni nokha m'Malawi News yalero.
account_circle
Onjezani Kenani(@onjezani) 's Twitter Profile Photo

I highly recommend Mibawa TV's Kanema m'manja app. We can now watch Mibawa's live television from any corner of the world.

account_circle
Onjezani Kenani(@onjezani) 's Twitter Profile Photo

N'chifukwa chiyani a Immigration akulandira ndalama za express passport chonsecho akudziwa kuti mwayi wa express palibe? That is theft by trick.

account_circle