@thambowillz
ID: 1095726047537086466
calendar_today13-02-2019 16:47:02
733 Tweet
1,1K Takipçi
1,1K Takip Edilen
5 hours ago
🔥The 9th Round of Easy Loan, Earn $40 Reward is in progress❗️ ⏰ Promotion Period: January 15th - Feburary 15th, 2025 👉 Register now and check more details at gate.io/campaigns/358
2 years ago
Usaziyike pa pressure,success yawo isakupatse mpanipani. There is one version of you!!!!, ulipo wekha!!!!
Get!! Well !! Soon !!!
Mwamuna sakhala ndi iPhone. Ameneyu ndi slay Queen
Koma bread opaka peyala kukoma kwakee eeeehhh
Koma anthu akunjoya eeeeeh. Ife tinabwera kuzaperekeza basi eeehhhh
Lero ndi tsiku limene Arsenal idziwe kuti Ovololo savalira lamba
Olo atandithira doom nkamwa sindinga sapote Arsenal. Newcastle all the way !!!!!
Kodi game ya Man City v R Madrid yatha bwanji? Ine ndimawonera ya Arsenal v Brighton yobwereza
Ndiye kuti apapa pali Arsenal pa top then Man U.. mmhh nice
Come watch the game with us! #ManchesterDerby #FACupFinal
Chinthu chatsala chokoma pa Malawi ndiku tokosa nkhutu basi
#TBT .... Arsenal pachanya also known as Arsenal pa Top pheeeee
Kungodziwama dzulo lero mwatumiza kale VN, mukuthamangira kuti ?
TBT
Koma izizi ndiziwanda eeeh. Kuwopa kusamba kuti ndikangosamba ndinyamuka eeeh ayi sizowona
Ha ha ha eish komanso zinthu zake ha ha ha
Kungoyakhula chizungu basi mwati aahh uyu sangakhale hule. Mhuu komatu pena pake amalawi.
8 months ago
10/10
Dope! Bless !